1 Mbiri 20:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Davide anatenga korona wa mfumu yao kumchotsa pamutu pake, napeza kulemera kwake talente wa golide; panalinso miyala ya mtengo wake pamenepo; ndipo anamuika pamutu pa Davide, natulutsa zankhondo za m'mzindamo zambiri ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Davide anatenga korona wa mfumu yao kumchotsa pamutu pake, napeza kulemera kwake talente wa golide; panalinso miyala ya mtengo wake pamenepo; ndipo anamuika pamutu pa Davide, natulutsa zankhondo za m'mudzimo zambiri ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Davide adaivula chisoti chagolide mfumu yao, ndipo atachiyesa, adapeza kuti chinkalemera makilogramu 5, ndipo pachisotipo panali mwala wamtengowapatali. Davide adachivala chisoticho, natenga zofunkha zochuluka mumzindamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Davide anachotsa chipewa chaufumu pamutu pa mfumu yawo. Chipewacho chinkalemera makilogalamu asanu agolide ndiponso chinali ndi miyala yokongola. Ndipo Davide anavala chipewacho. Iye anatenga katundu wambiri kuchokera mu mzindawo, Onani mutuwo |