Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 2:54 - Buku Lopatulika

54 Ana a Salima: Betelehemu, ndi Anetofa, Ataroti-Beti-Yowabu, ndi Hazi Amanahati, ndi Azori.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

54 Ana a Salima: Betelehemu, ndi Anetofa, Ataroti-Beti-Yowabu, ndi Hazi Amanahati, ndi Azori.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

54 Ana a Salima naŵa: Betelehemu, Anetofa, Ataroti-Beti-Yowabu ndi hafu la Amanahati, ndiponso Azori.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

54 Zidzukulu za Salima zinali izi: Betelehemu, Anetofati, Atiroti-Beti-Yowabu, theka la banja la Manahati, Azori,

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 2:54
12 Mawu Ofanana  

Helebi mwana wa Baana Mnetofa, Itai mwana wa Ribai wa ku Gibea wa ana a Benjamini;


Maharai Mnetofa, Heledi mwana wa Baana Mnetofa,


Ndipo Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu anali ndi ana: Harowe, ndi Hazi Amenuwoti.


Ndi mabanja a Kiriyati-Yearimu: Aitiri, ndi Aputi, ndi Asumati, ndi Amisrai; Azorati ndi Aestaoli anafuma kwa iwowa.


Ndi mabanja a alembi okhala ku Yabezi: Atirati, Asimeati, Asukati. Iwo ndiwo Akeni ofuma ku Hamati, kholo la nyumba ya Rekabu.


ndi Penuwele atate wa Gedori, ndi Ezere atate wa Husa. Awa ndi ana a Huri woyamba wa Efurata atate wa Betelehemu.


ndi Obadiya mwana wa Semaya, mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni, ndi Berekiya mwana wa Asa, mwana wa Elikana, wokhala m'midzi ya Anetofa.


Anthu a ku Netofa, makumi asanu mphambu asanu ndi mmodzi.


Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,


Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu.


natuluka ku Betele kunka ku Luzi, napitirira kunka ku malire a Aariki, ku Ataroti;


Ndipo masiku akuweruza oweruzawo munali njala m'dziko. Ndipo munthu wa ku Betelehemu ku Yuda anamuka nakagonera m'dziko la Mowabu, iyeyu, ndi mkazi wake, ndi ana ake aamuna awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa