Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 2:53 - Buku Lopatulika

53 Ndi mabanja a Kiriyati-Yearimu: Aitiri, ndi Aputi, ndi Asumati, ndi Amisrai; Azorati ndi Aestaoli anafuma kwa iwowa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 Ndi mabanja a Kiriyati-Yearimu: Aitiri, ndi Aputi, ndi Asumati, ndi Amisrai; Azorati ndi Aestaoli anafuma kwa iwowa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 Mabanja a Kiriyati-Yearimu naŵa: Aitiri, Aputi, Asumati ndi Amisirai. Ameneŵa ndiwo makolo a Azorati ndi Aesitaoli.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 ndipo mabanja a Kiriati-Yeyarimu anali awa: Aitiri, Aputi, Asumati ndi Amisirai. Azorati ndi Aesitaoli anachokera kwa amenewa.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 2:53
11 Mawu Ofanana  

Ira Mwitiri, Garebu Mwitiri;


Ira Mwitiri, Garebu Mwitiri,


Ndipo Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu anali ndi ana: Harowe, ndi Hazi Amenuwoti.


Ana a Salima: Betelehemu, ndi Anetofa, Ataroti-Beti-Yowabu, ndi Hazi Amanahati, ndi Azori.


Ndipo Reaya mwana wa Sobala anabala Yahati; ndi Yahati anabala Ahumai, ndi Lahadi. Iwo ndiwo mabanja a Azorati.


Ku chigwa, Esitaoli, ndi Zora ndi Asina;


Ndipo malire a cholowa chao anali Zora, ndi Esitaoli, ndi Irisemesi;


Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, nafika kumizinda yao tsiku lachitatu. Koma mizinda yao ndiyo Gibiyoni, ndi Kefira, ndi Beeroti ndi Kiriyati-Yearimu.


Ndipo panali munthu wina wa Zora wa banja la Adani, dzina lake ndiye Manowa; ndi mkazi wake analibe mwana, sanabale.


Ndipo mzimu wa Yehova unayamba kumfulumiza mtima ku misasa ya Dani pakati pa Zora ndi Esitaoli.


Pamenepo anatsika abale ake ndi banja lonse la atate wake, namnyamula, nakwera naye, namuika pakati pa Zora ndi Esitaoli, m'manda a Manowa atate wake. Ndipo adaweruza Israele zaka makumi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa