1 Mbiri 2:52 - Buku Lopatulika52 Ndipo Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu anali ndi ana: Harowe, ndi Hazi Amenuwoti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Ndipo Sobala atate wa Kiriyati-Yearimu anali ndi ana: Harowe, ndi Hazi Amenuwoti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Sobala bambo wake wa Kiriyati-Yearimu adaberekanso ana ena, naŵa: Harowe, ndiye kuti theka la Amenuwoti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Zidzukulu za Sobala abambo a Kiriati Yearimu zinali izi: Harowe, theka la banja la Manahati, Onani mutuwo |