1 Mbiri 2:44 - Buku Lopatulika44 Ndi Sema anabala Rahama atate wa Yorikeamu, ndi Rekemu anabala Samai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Ndi Sema anabala Rahama atate wa Yorikeamu, ndi Rekemu anabala Samai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Sema adabereka Rahama, bambo wake wa Yorikeamu ndipo Rekemu adabereka Samai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Sema anali abambo ake Rahamu ndipo Rahamu anali abambo a Yorikeamu. Rekemu anali abambo a Samai. Onani mutuwo |