1 Mbiri 2:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo Sesani analibe ana aamuna, koma ana aakazi. Ndi Sesani anali naye mnyamata Mwejipito dzina lake ndiye Yara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo Sesani analibe ana amuna, koma ana akazi. Ndi Sesani anali naye mnyamata Mwejipito dzina lake ndiye Yara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Sesani analibe ana aamuna, anali ndi ana aakazi okhaokha. Koma anali ndi kapolo wake wa ku Ejipito, dzina lake Yara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Sesani sanabereke ana aamuna koma aakazi okhaokha. Iye anali ndi wantchito wa ku Igupto, dzina lake Yariha. Onani mutuwo |