1 Mbiri 2:18 - Buku Lopatulika18 Ndi Kalebe mwana wa Hezironi anabala ana ndi Azuba mkazi wake, ndi Yerioti; ndipo ana ake ndiwo Yesere, ndi Sobabu, ndi Aridoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi Kalebe mwana wa Hezironi anabala ana ndi Azuba mkazi wake, ndi Yerioti; ndipo ana ake ndiwo Yesere, ndi Sobabu, ndi Aridoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Kalebe mwana wa Hezironi anali nawo ana omubalira mkazi wake Azuba ndiponso Yerioti. Ana amene adabala mkaziyo naŵa: Yesere, Sobabu ndi Aridoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kalebe mwana wa Hezironi anabereka ana mwa Azuba mkazi wake (ndi mwa Yerioti). Ana a mkaziyo anali awa: Yeseri, Sobabu ndi Aridoni. Onani mutuwo |