Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 2:10 - Buku Lopatulika

10 Ndi Ramu anabala Aminadabu; ndi Aminadabu anabala Nasoni kalonga wa ana a Yuda;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndi Ramu anabala Aminadabu; ndi Aminadabu anabala Nasoni kalonga wa ana a Yuda;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ramu adabereka Aminadabu, Aminadabu adabereka Nasoni, mkulu wa fuko la Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ramu anabereka Aminadabu ndipo Aminadabu anali abambo ake a Naasoni, mtsogoleri wa fuko la Yuda.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 2:10
11 Mawu Ofanana  

ndi Nasoni anabala Salimoni, ndi Salimoni anabala Bowazi,


Ndi ana a Hezironi anambadwirawo: Yerameele, ndi Ramu, ndi Kalebe.


Ndipo Aroni anadzitengera Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Nasoni, akhale mkazi wake; ndipo anambalira Nadabu ndi Abihu, Eleazara ndi Itamara.


Wa Yuda, Nasoni mwana wa Aminadabu.


Ndipo anayamba kuyenda ambendera ya chigono cha ana a Yuda monga mwa magulu ao; woyang'anira gulu lake ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu.


Ndipo iwo akumanga mahema ao ku m'mawa kotuluka dzuwa ndiwo a mbendera ya chigono cha Yuda, monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana Yuda ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu.


Wakubwera nacho chopereka chake tsiku loyamba ndiye Nasoni mwana wa Aminadabu, wa fuko la Yuda:


ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Nasoni mwana wa Aminadabu.


ndi Ramu anabala Aminadabu; ndi Aminadabu anabala Nasoni; ndi Nasoni anabala Salimoni;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa