Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 18:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo pakumva Tou, mfumu ya ku Hamati, kuti Davide adakantha khamu lonse la Hadadezere mfumu ya ku Zoba,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo pakumva Tou, mfumu ya ku Hamati, kuti Davide adakantha khamu lonse la Hadadezere mfumu ya ku Zoba,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Pamene Tou mfumu ya ku Hamati adamva kuti Davide wagonjetsa gulu lonse la ankhondo la Hadadezere, mfumu ya ku Zoba,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Tou, mfumu ya Hamati atamva kuti Davide wagonjetsa gulu lonse lankhondo la Hadadezeri mfumu ya Zoba,

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 18:9
4 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene Toi mfumu ya ku Hamati anamva kuti Davide adakantha khamu lonse la Hadadezere,


anatumiza Hadoramu mwana wake kwa mfumu Davide, kumlonjera ndi kumdalitsa, popeza adayambana ndi Hadadezere, namkantha; pakuti Hadadezere adachita nkhondo ndi Tou; ndipo anali nazo zipangizo za mitundumitundu za golide ndi siliva ndi mkuwa.


Ndi ku Tibati, ndi ku Kuni, mizinda ya Hadadezere, Davide anatenga mkuwa wambiri, ndiwo umene Solomoni anayenga nao thawale lamkuwa, ndi nsanamira, ndi zipangizo zamkuwa.


Ndipo pamene ana a Amoni anaona kuti anadzinunkhitsa kwa Davide, Hanuni ndi ana a Amoni anatumiza matalente chikwi chimodzi a siliva, kudzilembera magaleta ndi apakavalo ku Mesopotamiya, ndi ku Aramu-Maaka, ndi ku Zoba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa