1 Mbiri 17:4 - Buku Lopatulika4 Kauze Davide mtumiki wanga, Atero Yehova, Usandimangire nyumba yokhalamo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Kauze Davide mtumiki wanga, Atero Yehova, Usandimangire nyumba yokhalamo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Kamuuze mtumiki wanga Davide kuti Ine Chauta ndikuti, Sudzandimangira ndiwe nyumba yoti ndizikhalamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Pita kamuwuze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova akunena kuti, sudzandimangira ndiwe nyumba yokhalamo.’ Onani mutuwo |