1 Mbiri 16:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo analowa nalo likasa la Mulungu, naliika pakati pa hemalo Davide adaliutsira; ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zoyamika pamaso pa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo analowa nalo likasa la Mulungu, naliika pakati pa hemalo Davide adaliutsira; ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zoyamika pamaso pa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Anthu adaloŵa nalo Bokosi lachipangano lija, nalikhazika pamalo pake m'kati mwa hema limene Davide adaamangira Bokosilo. Tsono adapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Iwo anabwera nalo Bokosi la Mulungu ndipo analiyika pamalo pake mʼkati mwa tenti imene Davide anayimika ndipo iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano pamaso pa Mulungu. Onani mutuwo |