Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 13:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo pamene anafika ku dwale la Kidoni, Uza anatambasula dzanja lake kulichirikiza likasa, pakuti ng'ombe zikadapulumuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo pamene anafika ku dwale la Kidoni, Uza anatambasula dzanja lake kulichirikiza likasa, pakuti ng'ombe zikadapulumuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Tsono atafika ku malo ophunthirapo tirigu ku Kidoni, ng'ombe zidaafuna kugwetsa Bokosi lija, ndiye Uza nkutambalitsa dzanja kuti aligwirire Bokosilo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Atafika pa malo opunthira tirigu ku Kidoni, Uza anatambalitsa dzanja lake kuti agwire bokosilo, chifukwa ngʼombe zinkafuna kugwa.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 13:9
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anafika pa dwale la Atadi, lili tsidya lija la Yordani, pamenepo anamlira maliro a atate wake masiku asanu ndi limodzi.


Ndipo pofika iwo ku dwale la Nakoni, Uza anatambasula dzanja lake, nachirikiza likasa la Mulungu; chifukwa ng'ombe zikadapulumuka.


Ansembenso, akuyandikiza kwa Yehova adzipatulitse, angawapasule Yehova.


Ndipo Yehova anati kwa iye, Muka, tsika; nukwere iwe ndi Aroni pamodzi ndi iwe; koma ansembe ndi anthu asapyole kukwera kwa Yehova, angawapasule.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa