1 Mbiri 13:14 - Buku Lopatulika14 Ndi likasa la Mulungu linakhala ndi banja la Obededomu m'nyumba mwake miyezi itatu; ndipo Yehova anadalitsa nyumba ya Obededomu, ndi zonse anali nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndi likasa la Mulungu linakhala ndi banja la Obededomu m'nyumba mwake miyezi itatu; ndipo Yehova anadalitsa nyumba ya Obededomu, ndi zonse anali nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Choncho Bokosi lachipanganolo lidakhala miyezi itatu kwa Obededomu, m'nyumba mwake. Ndipo Chauta adadalitsa banja la Obededomu pamodzi ndi zonse zimene adaali nazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndipo Bokosi la Mulungu linakhala mʼbanja la Obedi-Edomu mʼnyumba mwake kwa miyezi itatu ndipo Yehova anadalitsa nyumba yake ndi chilichonse chimene anali nacho. Onani mutuwo |