Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 12:7 - Buku Lopatulika

7 ndi Yowela, ndi Zebadiya, ana a Yerohamu wa ku Gedori.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 ndi Yowela, ndi Zebadiya, ana a Yerohamu wa ku Gedori.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Panalinso Yowela ndi Zebadiya, ana a Yerohamu wa ku Gedori.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 ndi Yowela ndi Zebadiya ana a Yerohamu wa ku Gedori.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 12:7
5 Mawu Ofanana  

Elikana, ndi Isiya, ndi Azarele, ndi Yowezere, ndi Yasobeamu ndiwo Akora;


Ndi Agadi ena anapatukira kwa Davide ku linga la m'chipululu, ngwazi zamphamvu zozerewera nkhondo, zogwira chikopa ndi mkondo; nkhope zao zikunga nkhope za mikango, ndi liwiro lao longa la ngoma mumapiri:


Ndi mkazi wake Myuda anabala Yeredi atate wa Gedori, ndi Hebere atate wa Soko, ndi Yekutiyele atate wa Zanowa. Ndipo awa ndi ana a Bitiya mwana wamkazi wa Farao, amene Meredi anamtenga.


Ndipo anamuka mpaka polowera ku Gedori kum'mawa kwa chigwa, kufunafuna podyetsa zoweta zao.


Halahulu, Betezuri, ndi Gedori,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa