1 Mbiri 12:4 - Buku Lopatulika4 ndi Isimaya wa ku Gibiyoni, wamphamvu mwa makumi atatuwo ndi woyang'anira makumi atatuwo, ndi Yeremiya, ndi Yahaziele, ndi Yohanani, ndi Yozabadi wa ku Gedera, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi Isimaya wa ku Gibiyoni, wamphamvu mwa makumi atatuwo ndi woyang'anira makumi atatuwo, ndi Yeremiya, ndi Yahaziele, ndi Yohanani, ndi Yozabadi wa ku Gedera, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 ndi Isimaya wa ku Gibiyoni, amene anali wamphamvu mwa anthu makumi atatu aja ndiponso mmodzi mwa atsogoleri ao. Panalinso Yeremiya, Yahaziele, Yohanani, Yozabadi wa ku Gedera, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 ndi Isimaiya wa ku Gibiyoni, munthu wamphamvu mʼgulu la anthu makumi atatu aja, yemwenso anali mtsogoleri wawo; Yeremiya, Yahazieli, Yohanani, Yozabadi wa ku Gederi, Onani mutuwo |