Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 12:3 - Buku Lopatulika

3 Mkulu wao ndiye Ahiyezere, ndi Yowasi, ana a Semaa wa ku Gibea; ndi Yeziyele, ndi Peleti, ana a Azimaveti; ndi Beraka, ndi Yehu wa ku Anatoti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mkulu wao ndiye Ahiyezere, ndi Yowasi, ana a Semaa wa ku Gibea; ndi Yeziyele, ndi Peleti, ana a Azimaveti; ndi Beraka, ndi Yehu wa ku Anatoti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Mtsogoleri wao anali Ahiyezere, wotsatana naye anali Yowasi. Aŵiri onsewo anali ana a Semaa wa ku Gibea. Panalinso Yeziyele ndi Peleti, ana a Azimaveti, Beraka, Yahu wa ku Anatoti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Mtsogoleri wawo anali Ahiyezeri ndi Yowasi ana a Semaya wa ku Gibeya; Yezieli ndi Peleti ana a Azimaveti; Beraka, Yehu wa ku Anatoti,

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 12:3
8 Mawu Ofanana  

Mutipatse ana ake aamuna asanu ndi awiri, ndipo tidzawapachika kwa Yehova mu Gibea wa Saulo, wosankhika wa Yehova. Mfumu niti, Ndidzawapereka.


Abiyaliboni Mwarabati, Azimaveti Mbahurimi;


Ira mwana wa Ikesi wa ku Tekowa, Abiyezere wa ku Anatoti,


Azimaveti Mbaharumi, Eliyaba Msaaliboni;


Anakoka mauta; naponya miyala, naponya mivi ndi uta ndi dzanja lamanja ndi lamanzere lomwe; ndiwo a abale ake a Saulo, Abenjamini.


ndi Isimaya wa ku Gibiyoni, wamphamvu mwa makumi atatuwo ndi woyang'anira makumi atatuwo, ndi Yeremiya, ndi Yahaziele, ndi Yohanani, ndi Yozabadi wa ku Gedera,


Ndi tsiku lachinai anasonkhana m'chigwa cha Beraka; pakuti pamenepo analemekeza Yehova; chifukwa chake anatcha dzina lake la malowo, Chigwa cha Beraka, mpaka lero lino.


Tsono mithengayo inafika ku Gibea kwa Saulo, nalankhula mau amenewa m'makutu a anthu; ndipo anthu onse anakweza mau, nalira misozi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa