1 Mbiri 12:2 - Buku Lopatulika2 Anakoka mauta; naponya miyala, naponya mivi ndi uta ndi dzanja lamanja ndi lamanzere lomwe; ndiwo a abale ake a Saulo, Abenjamini. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Anakoka mauta; naponya miyala, naponya mivi ndi uta ndi dzanja lamanja ndi lamanzere lomwe; ndiwo a abale ake a Saulo, Abenjamini. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Iwoŵa anali anthu odziŵa kugwiritsa ntchito uta. Mivi ndi miyala ankatha kuponyera dzanja lamanja kapena lamanzere. Iwoŵa anali Abenjamini, abale ake a Saulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iwo anali ndi mauta ndipo amadziwa kuponya mivi komanso miyala, ndipo amatha kuponyera dzanja lamanja kapena lamanzere. Iwo anali abale ake a Sauli ochokera ku fuko la Benjamini. Onani mutuwo |