1 Mbiri 12:1 - Buku Lopatulika1 Anadzawo kwa Davide ku Zikilagi, akali chitsekedwere chifukwa cha Saulo mwana wa Kisi, ndi awa; ndiwo mwa amphamvuwo omthandiza kunkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Anadzawo kwa Davide ku Zikilagi, akali chitsekedwere chifukwa cha Saulo mwana wa Kisi, ndi awa; ndiwo mwa amphamvuwo omthandiza kunkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Naŵa anthu amene adadza kwa Davide ku Zikilagi, kumene Davideyo adaathaŵira chifukwa choopa Saulo mwana wa Kisi. Anthu ameneŵa ankathandiza Davide kumenya nkhondo, pamodzi ndi anzao amphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Nawa anthu amene anabwera kwa Davide ali ku Zikilagi pamene iye anathamangitsidwa ndi Sauli mwana wa Kisi (iwowo anali mʼgulu la asilikali amene ankamuthandiza pa nkhondo. Onani mutuwo |