1 Mbiri 11:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anamanga mzinda pozungulira pake, kuyambira ku Milo ndi pozungulira pake; ndi Yowabu anakonzanso potsala pa mzinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anamanga mudzi pozungulira pake, kuyambira ku Milo ndi pozungulira pake; ndi Yowabu anakonzanso potsala pa mudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndipo adamanga mzinda kuzungulira deralo kuyambira ku linga la Milo mpaka m'kati mwake. Yowabu ndiye adakonza mbali ina ya mzindawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye anamanga malo onse ozungulira, kuyambira ku matsitso ozungulira khoma. Ndipo Yowabu anakonzanso mbali ina ya mzindawu. Onani mutuwo |