Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 11:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo Davide anakhala m'lingamo; chifukwa chake analitcha mzinda wa Davide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo Davide anakhala m'lingamo; chifukwa chake analitcha mudzi wa Davide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Popeza kuti Davide ankakhala m'lingamo, lingalo linkatchedwa Mzinda wa Davide.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Tsono Davide anakhazikika mu lingamo, ndipo mzindawu anawutcha Mzinda wa Davide.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 11:7
5 Mawu Ofanana  

Chinkana anatero Davide anathyola linga la Ziyoni, lomwelo ndilo mzinda wa Davide.


Ndipo nzika za mu Yebusi zinati kwa Davide, Sungalowe muno. Koma Davide analanda linga la Ziyoni, ndiwo mzinda wa Davide.


Nati Davide, Aliyense woyamba kukantha Ayebusi, yemweyo adzakhala mkulu ndi mtsogoleri. Nayamba kukwerako Yowabu mwana wa Zeruya, nakhala mkulu iyeyu.


Ndipo anamanga mzinda pozungulira pake, kuyambira ku Milo ndi pozungulira pake; ndi Yowabu anakonzanso potsala pa mzinda.


Koma Ine ndadzoza mfumu yanga Pa Ziyoni, phiri langa loyera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa