1 Mbiri 10:6 - Buku Lopatulika6 Momwemo anafa Saulo, ndi ana ake atatu; ndi nyumba yake yonse idafa pamodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Momwemo anafa Saulo, ndi ana ake atatu; ndi nyumba yake yonse idafa pamodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Umu ndimo m'mene adafera Saulo, iyeyo ndi ana ake atatu, pamodzi ndi banja lake lonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Motero Sauli ndi ana ake atatu anafa, pamodzi ndi banja lake lonse anafera limodzi. Onani mutuwo |