Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 10:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo pamene wonyamula zida zake anaona kuti Saulo wafa, anagwera nayenso lupanga lake, nafa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo pamene wonyamula zida zake anaona kuti Saulo wafa, anagwera nayenso lupanga lake, nafa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Wonyamula zida uja ataona kuti Sauloyo wafa, nayenso adadzigwetsa pa lupanga lake, nkufa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mnyamata wonyamula zida zake uja ataona kuti Sauli wafa, nayenso anadzigwetsera pa lupanga lake nafa.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 10:5
4 Mawu Ofanana  

Pamenepo Saulo anati kwa wonyamula zida zake, Solola lupanga lako, nundipyoze nalo, angafike osadulidwa awa ndi kundiseka. Koma wonyamula zida zake anakana, popeza anaopa kwambiri. Pomwepo Saulo anatenga lupanga lake, naligwera.


Momwemo anafa Saulo, ndi ana ake atatu; ndi nyumba yake yonse idafa pamodzi.


Pamenepo anaitana msanga mnyamata wake wosenza zida zake, nanena naye, Solola lupanga lako nundiphe, angamanenere anthu, ndi kuti, Anamupha ndi mkazi. Nampyoza mnyamata wake, nafa iye.


Ndipo pakuona kuti Saulo anafa, wonyamula zida zake yemwe, anagwera lupanga lake, nafera limodzi ndi iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa