1 Mbiri 10:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anaika zida zake m'nyumba ya milungu yao, napachika mutu wake m'nyumba ya Dagoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anaika zida zake m'nyumba ya milungu yao, napachika mutu wake m'nyumba ya Dagoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono adaika zida za Sauloyo m'nyumba ya milungu yao, ndipo adakhomerera mutu wakewo ku nyumba ya Dagoni, mulungu wao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iwo anayika zida zake zankhondo mʼnyumba zopembedzera milungu yawo ndipo anapachika mutu wake mʼnyumba ya Dagoni. Onani mutuwo |