1 Mbiri 10:1 - Buku Lopatulika1 Afilisti tsono analimbana nkhondo ndi Israele; ndipo amuna a Israele anathawa pamaso pa Afilisti, nagwa ophedwa paphiri la Gilibowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Afilisti tsono analimbana nkhondo ndi Israele; ndipo amuna a Israele anathawa pamaso pa Afilisti, nagwa ophedwa pa phiri la Gilibowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Afilisti adamenyananso nkhondo ndi Aisraele, ndipo Aisraele adathaŵa Afilisti; ambiri adakaphedwa ku phiri la Gilibowa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsono Afilisti anachitanso nkhondo ndi Aisraeli ndipo Aisraeli anathawa Afilistiwo, kotero kuti ambiri anaphedwa pa phiri la Gilibowa. Onani mutuwo |