Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 1:54 - Buku Lopatulika

54 mfumu Magadiele, mfumu Iramu. Awa ndi mafumu a Edomu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

54 mfumu Magadiele, mfumu Iramu. Awa ndi mafumu a Edomu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

54 Magadiele ndi Iramu. Ameneŵa ndiwo mafumu a ku Edomu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

54 Magidieli ndi Iramu. Awa anali mafumu a ku Edomu.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 1:54
4 Mawu Ofanana  

Amenewa ndi mafumu a ana aamuna a Esau: ana aamuna a Elifazi woyamba wa Esau: mfumu Temani, mfumu Omara, mfumu Zefo, mfumu Kenazi,


mfumu Kenazi, mfumu Temani, mfumu Mibizara;


Ana a Israele ndi awa: Rubeni, Simeoni, Levi, ndi Yuda, Isakara, ndi Zebuloni,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa