Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 1:53 - Buku Lopatulika

53 mfumu Kenazi, mfumu Temani, mfumu Mibizara;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 mfumu Kenazi, mfumu Temani, mfumu Mibizara;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 Kenazi, Temani, Mibizara,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 Kenazi, Temani, Mibezari,

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 1:53
5 Mawu Ofanana  

Ndipo ana aamuna a Elifazi ndiwo Temani, Omara, Zefo ndi Gatamu, ndi Kenazi.


Ana a Elifazi: Temani, ndi Omara, Zefi, ndi Gatamu, Kenazi, ndi Timna, ndi Amaleke.


mfumu Oholibama, mfumu Ela, mfumu Pinoni;


mfumu Magadiele, mfumu Iramu. Awa ndi mafumu a Edomu.


Za Edomu. Yehova wa makamu atero: Kodi mu Temani mulibenso nzeru? Kodi uphungu wawathera akuchenjera? Kodi nseru zao zatha psiti?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa