1 Mbiri 1:51 - Buku Lopatulika51 Namwalira Hadadi. Ndipo mafumu a Edomu ndiwo mfumu Timna, mfumu Aliva, mfumu Yeteti; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Namwalira Hadadi. Ndipo mafumu a Edomu ndiwo mfumu Timna, mfumu Aliva, mfumu Yeteti; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Hadadi nayenso nkufa. Mafumu a ku Edomu anali aŵa: Timna, Aliva, Yeteti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Hadadi anamwaliranso. Mafumu a ku Edomu anali: Timna, Aliva, Yeteti, Onani mutuwo |