1 Mbiri 1:41 - Buku Lopatulika41 Mwana wa Ana: Disoni. Ndi ana a Disoni: Hamurani, ndi Esibani, ndi Itirani, ndi Kerani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Mwana wa Ana: Disoni. Ndi ana a Disoni: Hamurani, ndi Esibani, ndi Itirani, ndi Kerani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Mwana wa Ana anali Disoni. Ana a Disoni naŵa: Hamurani, Esibani, Itirani, ndi Kerani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Mwana wa Ana anali Disoni. Ana a Disoni anali awa: Hemudani, Esibani, Itirani ndi Kerani Onani mutuwo |