Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 1:34 - Buku Lopatulika

34 Ndipo Abrahamu anabala Isaki. Ana a Isaki: Esau, ndi Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Ndipo Abrahamu anabala Isaki. Ana a Isaki: Esau, ndi Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Abrahamu adabereka Isaki. Ana a Isaki naŵa: Esau ndi Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Abrahamu anabereka Isake. Ana a Isake anali awa: Esau ndi Israeli.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 1:34
12 Mawu Ofanana  

Mibadwo ya Isaki mwana wake wa Abrahamu ndi iyi: Abrahamu anabala Isaki:


Ndipo anati, Dzina lako silidzatchedwanso Yakobo, koma Israele, chifukwa unayesana naye Mulungu ndithu, ndipo unapambana.


Yakobo ndipo anafunsa iye, nati, Undiuze ine dzina lako. Ndipo iye anati, Undifunsa dzina chifukwa ninji? Ndipo anamdalitsa iye pamenepo.


Ana a Abrahamu: Isaki, ndi Ismaele.


Ndi ana a Midiyani: Efa, ndi Efere, ndi Hanoki, ndi Abida, ndi Elida. Awa onse ndiwo ana a Ketura.


Abrahamu anabala Isaki; ndi Isaki anabala Yakobo; ndi Yakobo anabala Yuda ndi abale ake;


mwana wa Yakobo, mwana wa Isaki, mwana wa Abrahamu, mwana wa Tera, mwana wa Nahori,


Ndipo anampatsa iye chipangano cha mdulidwe; ndipo kotero Abrahamu anabala Isaki, namdula tsiku lachisanu ndi chitatu; ndi Isaki anabala Yakobo, ndi Yakobo anabala makolo aakulu aja khumi ndi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa