Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 1:23 - Buku Lopatulika

23 ndi Ofiri, ndi Havila, ndi Yobabu. Awa onse ndiwo ana a Yokotani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 ndi Ofiri, ndi Havila, ndi Yobabu. Awa onse ndiwo ana a Yokotani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onseŵa anali ana a Yokotani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onsewa anali ana aamuna a Yokitani.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 1:23
12 Mawu Ofanana  

ndi Ofiri ndi Havila, ndi Yobabu; onse amenewa ndi ana a Yokotani.


Dzina la woyamba ndi Pisoni: umenewo ndiwo wozungulira dziko lonse la Havila, m'mene muli golide;


Ndipo anakhala iwo kuyambira ku Havila kufikira ku Suri, ndiko kum'mawa kwake kwa Ejipito, pakunka ku Asiriya: ndipo iye anakhala pamaso pa abale ake onse.


Ndipo zombo za Hiramu zotengera golide ku Ofiri zinatenganso ku Ofiri mitengo yambiri yambawa, ndi timiyala ta mtengo wapatali.


Ndipo iwo anafika ku Ofiri, natengako golide matalente mazana anai mphambu makumi awiri, nafika naye kwa mfumu Solomoni.


ndi Ebala, ndi Abimaele, ndi Sheba,


Semu, Aripakisadi, Sela;


ndicho matalente zikwi zitatu za golide, golide wa Ofiri; ndi matalente zikwi zisanu ndi ziwiri a siliva woyengetsa, kumamatiza nazo makoma a nyumbazi;


Ndipo utaye chuma chako kufumbi, ndi golide wa ku Ofiri ku miyala ya kumitsinje.


Mwa omveka anu muli ana aakazi a mafumu; ku dzanja lanu lamanja aima mkazi wa mfumu wovala golide wa ku Ofiri.


Ndipo ndidzachepsa anthu koposa golide, ngakhale anthu koposa golide weniweni wa ku Ofiri.


Ndipo Saulo anakantha Aamaleke, kuyambira pa Havila, dera la ku Suri, chili pandunji pa Ejipito.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa