Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 1:13 - Buku Lopatulika

13 Ndi Kanani anabala Sidoni mwana wake woyamba, ndi Heti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndi Kanani anabala Sidoni mwana wake woyamba, ndi Heti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Kanani adabereka Sidoni mwana wake wachisamba ndi Heti.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Kanaani anabereka mwana wake wachisamba Sidoni, ndipo anaberekanso Ahiti,

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 1:13
13 Mawu Ofanana  

Ndipo ana a Hiti analimbitsira Abrahamu munda, ndi phanga lili m'menemo, likhale lake lamanda.


Ndipo Abrahamu anauka pa wakufa wake, nanena kwa ana a Hiti, nati,


Ndipo ana a Hiti anayankha Abrahamu nati kwa iye,


Ndipo anati Rebeka kwa Isaki, Ndalema moyo wanga chifukwa cha ana aakazi a Ahiti, akatenga Yakobo mkazi wa ana aakazi a Ahiti, onga ana aakazi a m'dziko lino, moyo wanga udzandikhalira ine bwanji?


Ndipo Hamu atate wake wa Kanani, anauona umaliseche wa atate wake, nauza abale ake awiri amene anali kunja.


Davide natumiza kwa Yowabu, nati, Unditumizire Uriya Muhiti. Ndipo Yowabu anatumiza Uriya kwa Davide.


ndi Apatirusi, ndi Akasiluhimu, (kumene anafuma Afilisti), ndi Akafitori.


ndi Ayebusi, ndi Aamori, ndi Agirigasi,


Ndipo ndidzatumiza mavu akutsogolere amene adzaingitsa Ahivi, Akanani, ndi Ahiti, pamaso pako.


Ndipo kunali, pakumva ichi mafumu onse a tsidya ilo la Yordani, kumapiri ndi kuchidikha, ndi ku madooko onse a Nyanja Yaikulu, pandunji pa Lebanoni: Ahiti ndi Aamori, Akanani, Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa