Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 1:12 - Buku Lopatulika

12 ndi Apatirusi, ndi Akasiluhimu, (kumene anafuma Afilisti), ndi Akafitori.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 ndi Apatirusi, ndi Akasiluhimu, (kumene anafuma Afilisti), ndi Akafitori.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Patirusimu, Kasiluhimu (kholo la Afilisti) ndi Kafitorimu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Apaturusi, Akasilu (kumene kunachokera Afilisti) ndi Akafitori.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 1:12
6 Mawu Ofanana  

ndi Patirusimu, ndi Kasiluhimu, m'menemo ndipo anatuluka Afilisti, ndi Kafitori.


Ndi Ejipito anabala Aludi, ndi Aanamimu, ndi Alehabu, ndi Anafituhimu,


Ndi Kanani anabala Sidoni mwana wake woyamba, ndi Heti,


chifukwa cha tsiku lakudzafunkha Afilisti onse, kuphera Tiro ndi Sidoni othangata onse akutsala; pakuti Yehova adzafunkha Afilisti, otsala a chisumbu cha Kafitori.


Kodi simukhala kwa Ine ngati ana a Kusi, inu ana a Israele? Ati Yehova. Sindinakweza Israele ndine, kumtulutsa m'dziko la Ejipito, ndi Afilisti ku Kafitori, ndi Aaramu ku Kiri?


Kunena za Aavimu akukhala m'midzi kufikira ku Gaza, Akafitori, akufuma ku Kafitori, anawaononga, nakhala m'malo mwao).


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa