Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 9:2 - Buku Lopatulika

2 Yehova anaonekera kwa Solomoni nthawi yachiwiri, monga momwe adamuonekera ku Gibiyoni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Yehova anaonekera kwa Solomoni nthawi yachiwiri, monga momwe adamuonekera ku Gibiyoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Chauta adamuwonekera kachiŵiri, monga momwe adaachitira ku Gibiyoni kuja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Yehova anamuonekera kachiwiri, monga momwe anamuonekera ku Gibiyoni.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 9:2
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova anakwiya ndi Solomoni, pokhala mtima wake unapatuka kwa Yehova Mulungu wa Israele, amene adamuonekera kawiri,


Ku Gibiyoni Yehova anaonekera Solomoni m'kulota usiku, nati Mulungu, Tapempha chimene ndikupatse.


Ndipo Yehova anaonekera kwa Solomoni usiku, nanena naye, Ndamva pemphero lako, ndadzisankhira malo ano akhale nyumba ya nsembe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa