1 Mafumu 9:13 - Buku Lopatulika13 Nati, Mizinda ino mwandipatsayi njotani, mbale wanga? Naitcha dzina lao, Dziko lachikole, kufikira lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Nati, Midzi yino mwandipatsayi njotani, mbale wanga? Naitcha dzina lao, Dziko lachikole, kufikira lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Nchifukwa chake adafunsa kuti, “Kodi iwe mbale wanga, monga ndi imeneyi mizinda imene wandipatsa?” Choncho imatchulidwa kuti dziko la Kabule mpaka lero lino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iye anafunsa kuti, “Mʼbale wanga, kodi iyi nʼkukhala mizinda yondipatsa?” Ndipo iye anayitcha mizindayo Dziko la Kabuli, dzina lomwe amatchedwa mpaka lero lino. Onani mutuwo |