1 Mafumu 9:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Hiramu anatuluka ku Tiro kukaona mizinda adampatsa Solomoniyo, koma siinamkomere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Hiramu anatuluka ku Tiro kukaona midzi adampatsa Solomoniyo, koma siinamkomera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Hiramu adabwera kuchokera ku Tiro kuti adzaone mizinda imene Solomoni adampatsa, koma sidamkondweretse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma Hiramu atabwera kuchokera ku Turo kudzaona mizinda imene Solomoni anamupatsa, sanasangalatsidwe nayo mizindayo. Onani mutuwo |