1 Mafumu 7:9 - Buku Lopatulika9 Izi zonse zinali za miyala ya mtengo wapatali yosemasema, malingana ndi miyeso yake, yocheka ndi mipeni ya manomano m'katimo ndi kunjako, kuyambira kumaziko kufikira kumutu, momwemonso kunjako ku bwalo lalikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Izi zonse zinali za miyala ya mtengo wapatali yosemasema, malingana ndi miyeso yake, yocheka ndi mipeni ya manomano m'katimo ndi kunjako, kuyambira kumaziko kufikira kumutu, momwemonso kunjako ku bwalo lalikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Zonsezi zidamangidwa ndi miyala yabwino kwambiri imene adaisema potsata miyeso yake yofunika, yochekedwa ndi sowo m'kati ndi kunja komwe. Miyala yotere adamangira nyumba kuchokera pa maziko mpaka pamwamba pa khoma, kuyambiranso m'bwalo la Nyumba ya Chauta mpaka ku bwalo lalikulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Nyumba zonsezi, kuyambira kunja mpaka ku bwalo lalikulu ndiponso kuchokera pa maziko mpaka pamwamba pa khoma, zinapangidwa ndi miyala yabwino kwambiri imene anayisema potengera miyeso yake yoyenera ndipo anayisalaza ndi macheka mʼkati ndi kunja komwe. Onani mutuwo |