1 Mafumu 7:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo makomo onse ndi mphuthu zonse zinali zaphwamphwa maonekedwe ake, ndipo zenera limodzi linapenyana ndi linzake mizere itatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo makomo onse ndi mphuthu zonse zinali zaphwamphwa maonekedwe ake, ndipo zenera limodzi linapenyana ndi linzake mizere itatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndipo makomo onse ndi mawindo omwe, mafuremu ake anali olingana monsemonse, m'litali mwake ndi m'mimba mwake, ndipo windo linkapenyana ndi windo linzake pa mizere itatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Zitseko zonse ndi mazenera omwe, maferemu ake anali ofanana mbali zonse. Mulitali mwake ndi mulifupi mwake, ndipo zenera linkapenyana ndi zenera linzake pa mizere itatu. Onani mutuwo |