1 Mafumu 7:41 - Buku Lopatulika41 Nsanamira ziwirizo, ndi mbale za mitu inali pamwamba pa nsanamira ziwirizo, ndi maukonde awiri ophimbira mbale ziwiri za mitu inali pamwamba pa nsanamirazo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Nsanamira ziwirizo, ndi mbale za mitu inali pamwamba pa nsanamira ziwirizo, ndi maukonde awiri ophimbira mbale ziwiri za mitu inali pamwamba pa nsanamirazo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 ndiye kuti kumanga nsanamira ziŵiri zija, kupanga ziwaya zokutira nsonga za makapotolosi okhala pamwamba pa nsanamirazo, ndiponso maukonde aŵiri aja ophimba ziwaya ziŵiri zija za kunsonga kw makapotolosi okhala pamwamba pa nsanamirazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 nsanamira ziwiri; mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo; maukonde awiri okongoletsera mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo; Onani mutuwo |