1 Mafumu 7:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo panali ngati mapewa anai pansi pangodya zinali za phaka limodzi, mapewawo anali a phaka lomwelo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo panali ngati mapewa anai pansi pangodya zinali za phaka limodzi, mapewawo anali a phaka lomwelo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Phaka lililonse linali ndi zigwiriro zinai, chigwiriro chimodzi pa ngodya iliyonse. Zigwirirozo zidapangidwira kumodzi ndi maphakawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Phaka lililonse linali ndi zogwirira zinayi; chogwirira chimodzi pa ngodya iliyonse, zolumikizidwa ku phakalo. Onani mutuwo |