Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 7:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo pamwamba pa nsanamirazo panali ngati akakombo malembedwe ake; motero anaitsiriza ntchito ya nsanamirazo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo pamwamba pa nsanamirazo panali ngati akakombo malembedwe ake; motero anaitsiriza ntchito ya nsanamirazo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Tsono pamwamba pa nsanamira zija adakongoletsapo ndi zosemasema zooneka ngati maluŵa a kakombo. Motero ntchito ya nsanamirazo idamalizika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Mitu ya pamwamba pa nsanamirazo inali yooneka ngati maluwa okongola kwambiri. Motero anamaliza ntchito ya nsanamirazo.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 7:22
4 Mawu Ofanana  

Ndipo mituyi inali pamwamba pa nsanamira za pa chipinda cholowera chinali ngati akakombo malembedwe ake, a mikono inai.


Ndipo anaimiritsa nsanamirazi pa chipinda cholowera cha Kachisi; naimiritsa nsanamira ya ku dzanja lamanja, natcha dzina lake Yakini; naimiritsa nsanamira yakumanzere, natcha dzina lake Bowazi.


Ndipo anayenganso thawale lamkuwa, kukamwa kwake kunali kwa mikono khumi, linali lozunguniza, ndi msinkhu wake unali mikono isanu; ndi chingwe cha mikono makumi atatu chinalizungulira.


Nsanamira ziwirizo, ndi mbale za mitu inali pamwamba pa nsanamira ziwirizo, ndi maukonde awiri ophimbira mbale ziwiri za mitu inali pamwamba pa nsanamirazo,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa