1 Mafumu 7:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo mituyi inali pamwamba pa nsanamira za pa chipinda cholowera chinali ngati akakombo malembedwe ake, a mikono inai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo mituyi inali pamwamba pa nsanamira za pa chipinda cholowera chinali ngati akakombo malembedwe ake, a mikono inai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono mitu imene inali pamwamba pa nsanamira m'khonde, inali itasemedwa ngati maluŵa a kakombo, kutalika kwake pafupifupi mamita aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mitu imene inali pamwamba pa nsanamira mʼkhonde inali yooneka ngati maluwa okongola kwambiri. Kutalika kwake kunali pafupifupi mamita awiri. Onani mutuwo |