Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 7:11 - Buku Lopatulika

11 Ndi pamwamba pake panali miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yosemasema monga muyeso wake, ndi mitengo yamkungudza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndi pamwamba pake panali miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yosemasema monga muyeso wake, ndi mitengo yamkungudza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ndipo pamwamba pake panalinso miyala yabwino kwambiri yosemedwa potsata miyeso yake yofunika, ndiponso pamwamba pa miyalayo panali matabwa amkungudza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Pamwamba pake panali pa miyala yabwino kwambiri, yosemedwa potengera miyeso yake. Pamwamba pa miyalayo panali matabwa a mkungudza.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 7:11
4 Mawu Ofanana  

Ndipo maziko ake anali a miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yaikulu, miyala ya mikono khumi, ndi miyala ya mikono isanu ndi itatu.


Ndipo bwalo lalikulu lozingapo linali ndi mizere itatu ya miyala yosemasema, ndi mzere umodzi wa mitanda yamkungudza, monga bwalo la pakati pa nyumba ya Yehova, ndi chipinda cholowera cha nyumbayo.


inunso ngati miyala yamoyo mumangidwa nyumba ya uzimu, kuti mukhale ansembe oyera mtima, akupereka nsembe zauzimu, zolandiridwa ndi Mulungu mwa Yesu Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa