1 Mafumu 7:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo maziko ake anali a miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yaikulu, miyala ya mikono khumi, ndi miyala ya mikono isanu ndi itatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo maziko ake anali a miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yaikulu, miyala ya mikono khumi, ndi miyala ya mikono isanu ndi itatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mazikowo adamangidwa ndi miyala yabwino kwambiri, yaikulu bwino, kutalika kwake inali mamita atatu ndi theka, ina mamita anai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Maziko ake anali a miyala yabwino kwambiri, kutalika kwa miyala ina kunali mamita atatu ndi theka, inanso mamita anayi. Onani mutuwo |