1 Mafumu 7:1 - Buku Lopatulika1 Koma nyumba ya iye yekha Solomoni anaimanga zaka khumi mphambu zitatu, natsiriza nyumba yake yonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma nyumba ya iye yekha Solomoni anaimanga zaka khumi mphambu zitatu, natsiriza nyumba yake yonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Solomoni adatha zaka khumi ndi zitatu akumanga nyumba yake yachifumu, ndipo adaimariza nyumba yonseyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Solomoni anamanga nyumba yake yaufumu kwa zaka 13. Onani mutuwo |