1 Mafumu 6:8 - Buku Lopatulika8 Khomo lolowera m'zipinda za pakati linali ku mbali ya ku dzanja lamanja ya nyumba; ndipo anthu amakwerera pa makwerero ozunguniza, kufikira ku zipinda za pakati, ndi kutuluka m'zapakatizo kulowa m'zachitatuzo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Khomo lolowera m'zipinda za pakati linali ku mbali ya ku dzanja lamanja ya nyumba; ndipo anthu amakwerera pa makwerero ozunguniza, kufikira ku zipinda za pakati, ndi kutuluka m'zapakatizo kulowa m'zachitatuzo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chipata choloŵera ku chipinda chapansi chija chinali chakumwera kwa Nyumbayo. Anthu ankachita kukwera makwerero pochoka ku chipinda chapansi kupita ku chipinda chapakati, chimodzimodzi pochoka ku chipinda chapakati kupita ku chipinda chapamwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Chipata cholowera ku chipinda chapansi chinali mbali ya kummwera kwa Nyumbayo. Panali makwerero okwerera ku chipinda chapakati ndiponso chipinda cha pamwamba. Onani mutuwo |