Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 6:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo m'nyumbamo anamanga mazenera a sefa wokhazikika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo m'nyumbamo anamanga mazenera a sefa wokhazikika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Adaika mawindo amene mafuremu ake anali oloŵa m'kati mwa makoma.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Anapanga mazenera amene maferemu ake anali olowa mʼkati mwa makoma a Nyumbayo.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 6:4
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anamanga chipinda cholowera pakhomo pa nyumba ya Kachisiyo, m'litali mwake munali mikono makumi awiri monga m'mimba mwake mwa nyumbayo, kupingasa kwake kunali mikono khumi ku khomo la nyumba.


Ndipo panali mazenera m'mizere itatuyo, zenera limodzi lopenyana ndi linzake mizere itatu.


Wokondedwa wanga akunga mphoyo, pena mwana wa mbawala: Taona, aima patseri pakhoma lathu. Apenyera pazenera, nasuzumira pamade.


Ndipo panali mazenera amkati okhazikika pazipinda ndi m'makoma a pakati pao, m'kati mwa chipata pozungulira ponse; momwemonso pamphuthu; ndipo panali mazenera pozungulira ponse m'katimo, ndi pa nsanamirazo panali akanjedza.


ziundo, ndi mazenera amkati okhazikika, ndi makonde am'mwamba akuzinga zipinda zosanjikizana zao zitatu, pandunji pa chiundo, otchinga ndi matabwa pozungulira pake, kuyambira pansi kufikira kumazenera; koma mazenera anaphimbika;


Ndipo panali mazenera amkati okhazikika, ndi akanjedza chakuno ndi chauko, kumbali zake za khonde; momwemonso pa zipinda za m'mphepete mwa nyumba, ndi pa matabwa ochindikira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa