1 Mafumu 5:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Hiramu anatumiza kwa Solomoni, nati, Ndazimva zija munatumiza kwa inezo, ndidzachita chifuniro chanu chonse, kunena za mitengo yamkungudza ndi mitengo yamlombwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Hiramu anatumiza kwa Solomoni, nati, Ndazimva zija munatumiza kwa inezo, ndidzachita chifuniro chanu chonse, kunena za mitengo yamkungudza ndi mitengo yamlombwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndipo adabweza mau kwa Solomoni akuti, “Ndamva zimene mwandipempha. Ndili wokonzeka kuchita zonse zimene mukufunazo, zoti anthu anga akudulireni mitengo ya mkungudza ndi ya paini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tsono Hiramu anabweza mawu awa kwa Solomoni: “Ndalandira uthenga umene mwanditumizira ndipo ine ndidzachita zonse zimene mukufuna pokupatsani mitengo ya mkungudza ndi payini. Onani mutuwo |