1 Mafumu 5:16 - Buku Lopatulika16 osawerenga akapitao a Solomoni akuyang'anira ntchito, ndiwo zikwi zitatu mphambu mazana atatu, amenewo analamulira anthu aja akugwira ntchito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 osawerenga akapitao a Solomoni akuyang'anira ntchito, ndiwo zikwi zitatu mphambu mazana atatu, amenewo analamulira anthu aja akugwira ntchito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Analinso ndi akapitao 3,300 amene ankayang'anira anthu ogwira ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 ndi akapitawo 33,000 amene ankayangʼanira ntchitoyi ndiponso anthu ogwira ntchito zina. Onani mutuwo |