1 Mafumu 5:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anawatuma ku Lebanoni mwezi umodzi zikwi khumi kuwasintha, mwezi umodzi iwo anali ku Lebanoni, miyezi iwiri anali kwao; ndipo Adoniramu anali kapitao wa athangata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anawatuma ku Lebanoni mwezi umodzi zikwi khumi kuwasintha, mwezi umodzi iwo anali ku Lebanoni, miyezi iwiri anali kwao; ndipo Adoniramu anali kapitao wa athangata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ankaŵatuma ku Lebanoni anthu 10,000 pamwezi, mosinthanasinthana. Ku Lebanoni ankakhalako mwezi umodzi, ndipo kwao ankakhalako miyezi iŵiri. Adoniramu ndiye amene ankayang'anira ntchito yathangatayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Iye ankatumiza anthu 10,000 ku Lebanoni pa mwezi mosinthanasinthana, kotero kuti ankakhala ku Lebanoniko mwezi umodzi ndipo kwawo ankakhalako miyezi iwiri. Adoniramu ndiye ankayangʼanira ogwira ntchito yathangatayo. Onani mutuwo |