1 Mafumu 5:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo mfumu Solomoni anasonkhetsa athangata mwa Aisraele onse, ndi athangatawo ndiwo anthu zikwi makumi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo mfumu Solomoni anasonkhetsa athangata mwa Aisraele onse, ndi athangatawo ndiwo anthu zikwi makumi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mfumu Solomoni adayambitsa ntchito yathangata m'dziko lonse la Israele. Ndipo anthu athangatawo analipo 30,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mfumu Solomoni inasonkhanitsa anthu ogwira ntchito ya thangata mʼdziko lonse la Israeli ndipo anthu athangatawo analipo 30,000. Onani mutuwo |